Boma kudzera kuunduna wa zofalitsa nkhani walamula bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) kuti lichotse chiletso choletsa kampani ya Multichoice Africa Holdings kukweza mitengo ya DStv. Nkhaniyi inayamba pa 21 July, 2023 pomwe kampani ya Multichoice kudzera pa masamba ake anchezo, inalengeza kuti kuyambira pa 1 August chaka chino, mitengo yomwe makasitomala amapeleka pogula […]
The post Boma lalamula MACRA kuchotsa chiletso pa mitengo yatsopano ya DStv appeared first on Malawi24.