Bambo wa zaka 32 yemwe anayambana ndi mkazi wake, ali m’manja mwa apolisi mu nzinda wa Lilongwe pomuganizira kuti amafuna kupha ana ake awiri powaponyera muchitsime cha madzi momwe akhalamo masiku atatu. Wofalitsa nkhani pa polisi ya Lilongwe Hastings Chigalu, wazindikira bamboyo ngati Aubrey Madzinkusamba yemwe amafuna kupha mwana wake wa mkazi wa zaka zisanu […]
The post Bambo wamangidwa poponyera ana ake awiri m’chitsime appeared first on Malawi 24.