Wolemba: Gracious Zinazi Bambo wa zaka 34 wanyongedwa lero lachitatu m'dziko la Singapore chifukwa chopezeka ndi mankhwala ozunguza ubongo a heroin okwana ma sipuni atatu mu chaka cha 2009. Bamboyu ndi Nagaenthran Dharmalingam, yemwe kwawo kwenikweni ndi ku Malaysia. Mayi ake komanso omuimirira pa mulandu anayesetsa kuti amupulumutse potenga ziletso komanso kufotokoza kuti ma lipoti […]
The post Bambo anyongedwa chifukwa chopezeka ndi mankhwala ozunguza ubongo mdziko la Singapore appeared first on Malawi 24.