Mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma ku Nyumba ya Malamulo a George Chaponda ati zomwe achita apolisi komanso anthu ena omwe alepheletsa ziwonetselo mu nzinda wa Lilongwe ndi m'chitidwe okupha ufulu wa nzika za dziko lino. A Chaponda anadzuka m'nyumba ya malamulo pamene zokambirana zinayamba ndipo anafunsa sipikala wa nyumbayi a Catherine Gotani Hara ngati zomwe […]
The post Apolisi akupha demokalase - Chaponda appeared first on Malawi 24.