Timu ya mizilazembe yomwe ikutsogolera 2024 TNM Super League m'dziko muno ya Silver Strikers kudzera kwa m'phunzitsi wake Peter Mponda yati timu ya Bullets singabwere pa khomo pawo kuti idzawononge mbiri yawo ya kusagonja chiyambileni ligi. Pambuyo pa masewelo amene aseweledwe loweluka pa bwalo la Silver pakati pa FCB Nyasa Big Bullets ndi Silver Strikers […]
The post A Bullets sangabwele kuti atiwonongele mbiri - Mponda appeared first on Malawi 24.