Mtumiki wa Mulungu Apostle Clifford Kawinga yemwe ndi m'tsogoleri wa Salvation For all Ministries International, akupitiliza ntchito yothandiza anthu osowa maka pa nthawi ino yomwe njala yafika posautsa m'dziko muno. A Kawinga dzulo apereka matumba 2000 a chimanga kwa mabanja 2000 m'dera la GVH Masuku, m'boma la Chiradzulu omwe akhudzidwa ndi njala. Iwowa anagawaso ma […]
The post Apostle Kawinga apereka chakudya kwa anthu 2000 omwe akhudzidwa ndi njala m'boma la Chiradzulu appeared first on Malawi 24.