Phungu wa ku Balaka West, Bertha Ndebele, wauza Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti anthu ku dera lake akugonera mango chifukwa chakusowa chakudya. A Ndebele, omwe ndi a chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) amayankhula izi kwa Phombeya ku Balaka pomwe a Chakwera pamodzi ndi mtsogoleri wa dziko la Mozambique a Filipe Nyusi […]
The post Anthu akugonera mango kuno, Phungu wa ku Balaka wauza a Chakwera appeared first on Malawi 24.