Nyimbo ya ‘Atambwali okhaokha’ ya Gibo Pearson ndi yomwe katswiri wosewera mpira wamiyendo, Khuda Myaba, akumvera pano kamba koti zoti banja lake latha ndi nkazi wake Enlecio, zinali nthabwala chabe ndipo wati iyeyo anakonda hule yemweyo. Lamulungu, Myaba anadzidzimutsa anthu pomwe analengeza kuti banja lake ndi osewera watimu ya Scorchers, Enlecio Mhango latha ponena kuti […]
The post Timangofuna tikuoneni – Khuda wati banja silinathe appeared first on Malawi 24.