Anthu pamasamba a mchezo ayamikira anthu a kwa Msakambewa ku Dowa chifukwa cha chikondi chomwe awonetsa pa mwana wa m'mudzi mwawo yemwe akukapitiriza maphunziro ku Israel. Anthu a kwa Msakambewa anatutana kupita ku bwalo lokwerera ndege la Kamuzu International kumuperekeza mwana wawoyi. Malingana ndi kanema yemwe akuyendayenda m'masamba a mchezo, anthuwa anasonkha ndalama yomwe amupasa […]
The post Anthu a ku Dowa awonetsa chikondi pa mwana yemwe akupita ku Israel appeared first on Malawi 24.