Pomwe anthu otsatira chipani cha People's (PP) anali ndi chimwemwe chodzadza tsaya kuti mwina mkutheka Mneneli David Mbewe awatengera mtsidya lina, munthu wa Mulunguyu watuluka mchipanichi atakhalamo maola ochepa. Mneneli Mbewe analowa chipani cha PP lachinayi pa 11 August ndipo mwambo omulandira mkuluyu unachitikira mu mzinda wa Lilongwe komwe akuluakulu achipani cha PP anati ndiosangalala […]
The post Mlendo ndimame sachedwa kukamuka: Mneneli Mbewe watuluka PP appeared first on Malawi 24.