Kaya ena akumalotabe nkumaganiza kuti adzachotsa chipani cha Malawi Congress m'boma, izi ayiwale kamba koti aChakwera akuti chipani chi chilowanso m'boma chaka cha m'mawa. A Chakwera amayankhula izi ku msonkhano waukukulu wa chipanichi ku Bingu International Convention Centre (BICC)-Lilongwe komwe amatseka msonkhano waukuluwu wa chipanichi. Mtsogoleri wa dziko linoyu anati mamembala achipanichi akuyenera kuchilimika pogwira […]
The post Olo wina afune, asafune MCP ilowanso m'boma - atero aChakwera appeared first on Malawi 24.