Mkwanda (L) Mawu a malemu pazisudzo John ‘Izeki' Nyanga oti ‘zina umangowona waziyamba' akuyankhulidwa mobwelezedwa ndi anyamata atatu osewera nkhonya mdziko muno kwinaku akuziguguda pachifuwa kuti unkalinda izi moyo wanga? Kaamba ka zibakera zomwe agagadidwa ku Zambia zomwe akuti zinawaonetsa dzenje lawo lamanda osati nyenyezi. Osewera nkhonya atatuwa omwe ndi Mussa ‘Boyker' Mkwanda, Agness Lewis […]
The post “Mukanamva ndamfera mu ring'i!” — walira wankhonya wa ku Malawi atagagadidwa ndi zibakera ku Zambia appeared first on Malawi24.