…akufuna madotolo kunja akamudule chiwalo chachimuna Wachisodzera wa zaka 21 yemwe anabadwa ndichiwalo chachikazi komaso chachimuna, wapempha anthu akufuna kwabwino kuti amuthandize kuti apite kunja kuti akamudule chiwalo chachimuna chomwe akuti chikumuzuza kwambiri. Wachisodzerayu yemwe munkhani ino timutchule kuti Mphatso, amayankhula izi pomwe amacheza ndi Rodwell Lumbe yemwe amachita utolankhani wa nzika ndipo wakhala akupangitsa […]
The post Wobadwa ndi ziwalo zobisika ziwiri akupempha thandizo appeared first on Malawi24.