Phungu wamdera la Chikwawa West Susan Dossi wati kuwonongeka kwa msewu ndi mlatho wa Chapananga kwapangitsa kuti anthu amdera lake adzivutika kwambiri pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku. Dossi wauza Malawi24 kuti anthu amdera lake akuvutika kupeza thandizo la za umoyo, alimi akuvutika kukagulitsa zokolola zawo komanso kugula feteleza chifukwa chakuwonongeka kwa msewu ndi mlatho. […]
The post Boma alipempha kuti likonze msewu ndi mlatho wa Chapananga appeared first on Malawi24.