Bungwe lomwe limawona za pamsewu la Directorate of Road Traffic and Safety Services (DRTSS) mchigawo chakum'mawa lalanda njinga zamoto 70 za anthu ochita bizinesi ya Kabanza mu mzinda wa Zomba zomwe zimayenda opanda chilolezo. Izi bungwelo lapanga monga akunenera malamulo oyendetsera ntchito za panseu ndime 11 ndime yaying'ono yachiwiri. (Section 11 sub section 2). M'modzi […]
The post DRTSS yalanda njinga zamoto 70 zopanda chilolezo ku Zomba appeared first on Malawi24.