Akatswili a zanyengo ati kuyambila lachitatu sabata lino, kubwela mvula ya mkuntho yoononga katundu. Malinga ndi chikalata chimene atulutsa ndipo chasainilidwa ndi mkulu wa nthambi yoona za nyengo mu dziko muno, a Jolam Nkhokwe, mvula ya mkunthoyi iyambila chigawo cha kummwela. Uthenga mu chikalatachi wati mvula imeneyi ikhala ikupambadza mpaka kufikila lamulungu, pa 28 November. […]
The post Konzekani, kukubwela mvula ndi mphepo zoononga – a za nyengo appeared first on Malawi 24.