Mkulu uja anaimba nyimbo zodzudzula misonkho yochuluka, anaimbanso zodzudzula tsankho, ndi kudzudzulanso kukonda ma ulendo kwa adindo, lero ati zinthu ku Malawi kuno sizinafike poipa pofuna kudzudzula. Lucius Banda amene ndi mlangizi wa President Lazarus Chakwera anauza anthu pa msonkhano wina wandale kuti asiye kukokomeza mavuto a ku Malawi kuno. 'Zinthu zikavuta mumaonela a nsembe […]
The post Sizinafike poipa zinthu, zikadzafika ndizaimba nyimbo - watelo Lucius Banda appeared first on Malawi 24.