Mpakana pano, anthu ena amaona ngati mankhwala amatenda a chifuwa chachikulu cha TB ndi ogulitsa zinthu zomwe adindo ati zakhala zikupangitsa ena mwa anthu odwala matendawa kuti asamalandire mankhwala mwandondomeko yoyenera komanso kusapita kolandira mankhwala kumene. Izi zadziwika pamene bungwe la African Institute for Development Policy (AFIDEP) mogwirizana ndi bungwe la Journalists Association Against AIDS […]
The post Mankhwala a chifuwa chachikulu cha TB ndi aulere – atero adindo appeared first on Malawi 24.