…akugonanso malo a nsikidzi… Aphunzitsi omwe akuchonga mayeso a Form 4 ku St Mary's Secondary School ku Zomba akunyanyala ntchito ati pofuna kukakamiza akulu akulu a MANEB kuti awapatse ndalama zawo zoyendera (transport) komanso ndalama zina zowonjezera. Mmodzi mwa aphunzitsiwa yemwe sadafune kuti timutchule dzina wati Bungwe la MANEB silidawapatsebe ndalama zawo zomwe adayendera ndipo […]
The post Aphunzitsi ochonga mayeso a Form 4 akunyanyala ntchito appeared first on Malawi 24.