Anthu anayi amwalira ndipo khumi awagonenka pachipatala cha Zomba Central Hospital m’boma la Zomba, atavulala pa ngozi yomwe yachitika lero m’bomalo. Malingana ndi aPolisi oyang’anira za pa nseu nchigawochi, a Augustine Chakanika ati ngoziyi yachitika pamene minibus yomwe anthuwa adakwera anagubuduzika kawiri pa 8 Miles m’bomali. A Chakanika ati ngoziyi yachitika kamba koti oyendetsa Minibus […]
The post Anthu anayi amwalira pa ngozi ku Zomba appeared first on Malawi 24.