Zatsimikizika kuti mamembala a bhodi ya timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers awachotsa. Wapampando wa timuyi a Thomson Mpinganjira atsimikiza za nkhaniyi. Mu chikalata chomwe wasayina ndi mtsogoleriyu chikufotoka kuti izi zadza kamba ka maganizo a akulualuku omwe ndi eni makampani omwe amathandizira kuyendetsa timuyi. 'Kamba ka kusinthidwa kwa adindowa, chilichose choyenera […]
The post Akuluakulu oyendetsa timu ya Wanderers awachotsa appeared first on Malawi 24.