“Ambuye wazatheka bwanji”; ngati nkhani ya Sarah mu bayibulo yemwe anabereka mwana atamera kale imvi, woyimba Jetu wakwera ndege kachiwiri pomwe watuluka m’dziko muno koyamba ali ndi zaka 72 kupita kokavinitsa anthu m’dziko la South Africa. Jetu, yemwe dzina lake lenileni ndi Christina Malaya, pamodzi ndi omuthandizira wake Emmu Dee, anyamuka lero chakum'mawaku kupita m'dziko […]
The post Jetu waotcha mtambo appeared first on Malawi 24.