Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre, akusunga m’chitokosi mzimayi wina wa zaka 21 chifukwa choononga paipi ya madzi a Blantyre Water Board mwadala ndicholinga choti atunge madzi aulele. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe a Aubrey Singanyama, mzimayi oganizilidwayu wazindikilidwa ngati a Celina Ganya omwe akuti anapalamula mlanduwu Lachiwiri sabata ino pa […]
The post Mayi wamangidwa pophwanya paipi yamadzi kuti atunge awulele appeared first on Malawi 24.