Oyimba Chipiliro Mwancheka wati iye sanathe ndipo atulutsa chimbale chatsopano chotchedwa 'Ndabwera' posachedwa. Chimbale chatsopano chimene akuyembekezera kutulutsa muli nyimbo zokwanira khumi ndipo zonse wayimba yekha. Nyimbo zisanu ndi zitatu wajambula yekha ku studio kwake pomwe ziwiri zajambulidwa ndi Viwe Chibwana, Dj Lobodo mothandizana ndi Banderous. Mwancheka wanenanso kuti nyimbo za tsopanozi waphatikizamo makhirikhiri chifukwa […]
The post 'Amene anatha ndiamene anamwalira munthu samatha ali moyo'- watero Chipiliro Mwancheka appeared first on Malawi 24.