Mtsogoleri wa zipani zotsutsa mu nyumba ya malamulo, Bambo Kondwani Nankhumwa, adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kamba kolephela dziko la Malawi. Polankhula mu nyumba ya malamulo, a Nankhumwa anati boma la a Chakwera lalephela. Mwa zina, iwo anatchulapo kukwela mitengo kwa zinthu ngati umboni wa kulephela kwa a Chakwera. A Nankhumwa anaonjezelapo […]
The post Ngati sali pa mseu, ali m’mwamba - Nankhumwa adzudzula Chakwera appeared first on Malawi 24.