‘Zangondipatsa minyama’: Ngati Saulo panjira ya ku Damasiko, m’modzi mwa anamatetule pa nyimbo za lokolo, Joe Gwaladi yemwe ali m’manja mwa apolisi, akuti watembenuka mtima ndipo pano akuti ayamba kuyimba nyimbo zauzimu. Gwaladi wayankhula izi lachinayi pomwe anthu ena akufuna kwabwino anakamuyendera ku polisi ya Phalombe komwe akusungidwa kamba kuganizilidwa kuti anavulaza wa chikondi wake […]
The post Gwaladi watembenuka mtima appeared first on Malawi 24.