M’modzi mwa akatswiri ochita zisudzo mdziko muno Andrea Thonyiwa amene amadziwika ndi dzina loti Mr Jokes, wapepesa kwaotsatira chipani chotsutsa cha DPP kaamba ka kanema yemwe anatulutsa oselewura momwe amayankhulira a Peter Mutharika. Mukanema yemwe anthu akugawana pamasamba amchezo ndipo tsamba lino tamuwona, akuonetsa katswiri ochita nthabwalayu akuyelekeza m’mene a Mutharika amayankhulira. Mkanemayu Mr Jokes […]
The post Mr Jokes apepesa poselewura a Mutharika appeared first on Malawi 24.