M'modzi mwa anthu omwe ali mkamwa mkamwa pano Dorothy Shonga, wasambwadza anthu onse omwe akuti akumamunyogodola zokhudza ubwezi wake ndi oyimba Zeze Kingston, ndipo waulura atsikana ambiri ali ndi zibwezi zochuluka. Nkhaniyi ikutsatira kubwera poyera kwa Shonga yemwe posachedwapa wadzidzimutsa anthu ochuluka podziwitsa dziko kuti ali m'chikondi ndi oyimba Zeze Kingston. Chigwereni m'chikondi ndi oyimbayu, […]
The post ‘Ana anjoka inu', Dorothy Shonga watopela omwe akumunyogodola za Zeze appeared first on Malawi24.