Mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizila a Malawi mdziko muno za kufunika kwa fodya ndi cholinga choti dziko lino likwanilitse maloto ake a 2063. Polankhula pa Vivya Primary School mdela la mfumu yaikulu Njombwa mboma la Kasungu, a Chakwera adati masomphenya a 2063, amalimbikitsa kufunika kochulukitsa ndalama. 'Tikamakamba za masomphenya a Malawi 2063, […]
The post Chakwera atsindika zakufunika kwa fodya kuti boma lake likwanilitse masomphenya 2063 appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.