Mayi wa fuko lino,Monica Chakwera yemwenso ndi kazembe pankhani yolimbana ndi matenda a chifuwa cha TB kuno ku Malawi akuyembekezeka kuyakhula nthumwi pa nkhani za umoyo zomwe zikusokhana mdziko la Switzerland komwe ali nawo pa msonkhano waukulu pa dziko lonse okambirana njira zolimbana ndi matenda a chifuwa cha chachikulu cha TB (World Health Summit). Madam […]
The post Madam Chakwera ali ku Switzerland ku msonkhano wokambirana zothesa matenda a TB appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.