Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera wati mtima wokonda kuyitanitsa katundu ku mayiko akunja womwe Amalawi ambiri ali nawo ndi umene ukulowetsa pansi chuma cha dziko lino. Chakwera ananena izi Lachitatu pamene amatsegulira chiwonetsero cha malonda mu mzinda wa Blantyre. Chiwonetsero cha malonda chimakonzedwa chaka chilichonse ndi bungwe la Malawi Confederation of Chambers […]
The post Mtima wokonda zakunja ukulowetsa pansi chuma chathu – Chakwera appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.