Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera agwira ntchito zosiyana siyana m'boma la Kasungu lero kuwonjezerapo kutsegulira m’sika wa fodya, malingana ndi chikalata watulutsa mlembi wamkulu wa boma mayi Colleen Zamba. A Chakwera akuyembekezeka kuyendera nyumba za asirikali a nkhondo zomwe boma la Malawi Congress (MCP) lamanga ku Engineering Battalion. Malingana ndi chikalatachi, mtsogoleri wa dziko […]
The post Chakwera atsekulira misika ya fodya ku Kasungu lero appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.