Bambo wa zaka 44 amumanga ku Mchinji chifukwa chogwirilira anyamata awiri a zaka zosaposera 12. Wofalitsa nkhani za apolisi ku Mchinji a Limbani Mpinganjira wati bamboyu dzina lake ndi James Makunganya. Malingana ndi a Mpinganjira, bamboyu aampereka K500 kwa anyamatawa komanso amawaopseza kuti awapha akakawulula kwa makolo awo. Koma anawa tsiku lina analimba mtima ndikuwawuza […]
The post Bambo wazaka 44 ali mchitokosi chifukwa chogwirilira anyamata appeared first on Malawi24.