Koma zilikotu. Ati chifukwa china mabanja sakulimba, kaya anthu kumangothibulana, ndi chifukwa choti anakhadzulirana nkhuku pa chinkhoswe. Watero mwini mpingo wa Fountain of Victory, a Joseph Ziba. Mu kanema amene wawanda tsopano, a Ziba amene amazitchula kuti ndi mpositoli ati mwambo wa chinkhoswe ndi njira imene ziwanda za a malume awo a anthu zimalowelera mu […]
The post Musiye kupanga chinkhoswe, ndi za ku midima izo zija - m'busa Joseph Ziba appeared first on Malawi 24.