Pomwe timu ya FCB Nyasa Big Bullets inali itapeleka kale K3 miliyoni ndipo imadikira kuti iwonetse kugulu katswiri wosewera kutsogolo mu timu ya Premier Bet Dedza Dynamos, Promise Kamwendo, osewerayu watikitira kontalakiti ku Mighty Mukuru Wanderers. Kamwendo yemwe lero Lolemba dzina lake linali pokopoko m’masamba a mchezo, wasayinira kontalakiti ya zaka zitatu ku Manoma ngakhale […]
The post Bullets yafa ndi imodzi pomwe Wanderers yasaina Kamwendo appeared first on Malawi 24.