Apolisi m'boma la Balaka amanga bambo wina, a Goodson Ali, a zaka 18 powaganizira kuti adagwirilira mwana wa zaka zisanu ndi zitatu (8). Malingana ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Balaka, Mphatso Munthali, bamboyu adachita izi pa 2 September, 2023 m'mudzi mwa Kambadi m'boma lomweli la Balaka. A Munthali adati bambo oganizilidwayu akuti adapempha […]
The post Bambo ali mchitokosi pa mulandu ogwirilira mwana wa zaka 8 appeared first on Malawi24.