Ndege imene anakwera wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Klaus Chilima yalephera kutela pa bwalo la ndege la Mzuzu chifukwa cha nyengo yoyipa yomwe ili munzindawu. Izi zakanikitsa a Chilima kukhala nawo pa mwambo woyika m’manda malemu Ralph Kasambara omwe ayikidwa mmanda tsiku la lero. Malingana ndi malipoti, a Chilima amayenela kukhala nawo […]
The post A Chilima akanika kutela pa bwalo la ndege la Mzuzu appeared first on Malawi 24.