Sukulu zomwe sizaboma zalangizidwa kuti ziyesetse kuti ndalama za nkhani nkhani zomwe ophunzira amapeleka ngati fizi zidzioneka phindu lake pokhozetsa bwino pa mayeso a boma, ponena kuti makolo amakhala atadutsa m'zikhomo kuti apeze ndalamazo. Izi ndimalingana ndi m’modzi mwa anthu odziwika bwino pa nkhani zopita pa tsogolo maphunziro m’dziko muno Ernest Kaonga omwe ati chimene […]
The post Yesetsani ndalama ya fizi idzioneka phindu lake - sukulu zomwe sizaboma zalangizidwa appeared first on Malawi 24.