Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wadzudzula ma kampane wena omwe amapatsidwa ntchito ya zomanga manga kuti akumachedwa kwambiri mukagwiridwe kawo ka ntchito. Mukulankhula kwawo, a Chakwera adati ndiwokhumudwa ndi m'mene ntchito zina za chitukuko zikuchedwera mdziko muno. A Chakwera alankhula izi lero boma la Rumphi komwe amatsekulira school zosula aziphuzitsi zomwe zamangidwa m'maboma […]
The post Walusa! Chakwera adzudzula ma kampane a zomanga manga kamba kochedwetsa ntchito appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.