Pomwe panali chiopsezo choti namondwe otchedwa Filipo atha kufika kuno ku Malawi, nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo m'dziko muno yati namondweyu tsopano wabwelera ku nyanja ya nchere ya India komwe anachokera, komabe yati mvula ya mphamvu ipitilirabe kugwa. Kumayambiliro kwa sabata ino nthambiyi inachenjeza kuti namondwe Filipo yemwe anafika mdziko la Mozambique Lamulungu […]
The post Namondwe Filipo wabwelera safika kuno, mvula ya mphavu ipitilira- atelo a za nyengo appeared first on Malawi 24.