Pomwe Mutale Mwanza wanenetsa kuti sanakhalepo pa ubwenzi ndi Tay Grin yemwe akuti ndi khanda komaso samatha kukonda mkazi, “mfumu ya zinyawu-yi” yati ikunong'oneza bondo posavera malangizo omwe anthu ankayipatsa kuti isachite chibwezi ndi nkazi wa ku Zambia-yu. Tay Grin yemwe dzina lake lenileni ndi Limbani Kalilani, walemba izi lero Lachiwiri pa tsamba lake la […]
The post Munandilangizadi aMalawi koma ine kusava - walira Tay Grin appeared first on Malawi 24.