Oweruza milandu Mzonde Mvula wayamba wayimitsa kaye kumva mlandu wa a Lester Maganga omwe akuwaganizira kuti anapha a Allan Witika mpakana pa 9 April chaka chino. Izi zili chomwechi chifukwa choti mboni ziwiri zaboma zomwe zimayenera kupelekera umboni sizinabwere. Bwaloli limayembekezeka kupitiliza kumva mlanduwu kuyambira lero kufikira lachinayi sabata ino. A Mvula atinso adzadziwitsa pa […]
The post Mulandu wa malemu Wittika: Khoti likumanaso lachiwiri mulungu wa mawa appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.