Mkaidi yemwe lachitatu anadabwitsa anthu kaamba kopezeka ndi mafoni awiri m'matumbo mwake kundende ya Zomba, wati analowetsa mafoniwa kudzera ku malo ochitila chimbudzi ndipo waulura kuti akaidi ambiri ali ndi anthu omwe amawapititsira mafoniwa kundendeko. Mkaidiyu yemwe dzina lake ndi Frank Siposi, lachitatu pa 11 May, 2022, m'mimba mwake munapezeka mafoni awiri othobwanya koma anyuwani, […]
The post Mkaidi awulura momwe analowetsera mafoni awiri m'matumbo mwake appeared first on Malawi 24.