Chipani cha People's (PP) chati tsogolo pa mgwirizano wake ndi zipani zina pansi pa mgwirizano wa Tonse udziwika kumapeto a chaka chino pamene chipanichi chikhale chikuchititsa msonkhano wake waukulu pa 7 September mu mzinda wa Lilongwe. Wofalitsa nkhani za chipanichi a Ackson Kalaile Banda wati nthumwi za chipanichi zokwana 400 ndi zomwe zidzakambirane ndi kugwirizana […]
The post Chipani cha PP chati chiziwa za tsogolo lake mu Tonse Alliance kumapeto kwa chaka chino appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.