Nthambi ya boma yowona njira zotengera madzi ya National Water Resources Authority yati mlingo wa madzi mu nyanja ya dziko lino wakwera kwambiri chaka chino poyerekeza ndi zaka za m'mbuyomu. Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa, mlingo wa madzi pofika pa 11 March chaka chino unali pa 475.95 meters omwe ndiokwera poyerekeza ndi mlingo wa […]
The post Chenjerani! Mlingo wa madzi wakwera kwambiri mu Lake Malawi appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.