…boma lawaonjezera malipiro ndi 41%…aloledwa kuitanitsa galimoto osakhomela msonkho Akakhala oweruza milandu zawo zoyera, za kukokanakokana timaziona ndi anamwino kapena ena oyendetsa galimoto zikulu-zikulu sizinaoneke kwenikweni. Ngakhale iwo eni oweruza milandu ayamika ndi kusintha kwa phindu lomwe azipeza akagwira ntchito tsopano. Patangotha sabata ziwiri a bwalo ataopseza kuti ayamba kunyanyala ntchito, boma lasintha malipiro ndi […]
The post Ayiphula oweruza milandu appeared first on Malawi 24.