A Polisi kwa Jenda m'boma la Mzimba amanga mayi wina ndi amuna awiri chifukwa chopezeka ndi fodya wa Chamba pamalo otchedwa Luviri m'bomali pomwe amadikira galimoto kuti apite ndi katunduyu ku Lilongwe. Malinga ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Jenda a Macfarlen Mseteka, atatuwa ndi a Pililani Phiri a zaka 46, a Stanley Mologeni a […]
The post A Polisi amanga mzimayi, abambo awiri kamba kopezeka ndi chamba appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.