Banki yaikulu pa dziko lonse ya World Bank yati chiwelengelo cha anthu osaukitsitsa chipitilila kuchuluka m'dziko muno ndi ma pelecenti 71.7 m'chaka cha 2023 kufika pa 72 pelecenti m'chaka cha 2024. Izi ndi malingana ndi kafukufuku yemwe banki-yi yachita ontchedwa Macro Poverty Outlook yemwe watuluka sabata yatha. Kafukufuku-yu akupeleka chithunzithunzi cha momwe mavuto alili komanso […]
The post A Malawi ambiri asauka kwambiri chaka chino mdziko muno kusiyana ndi chaka chatha, yatero World Bank appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.