Nduna yowona za Mauthenga ndi Makina a Digito m'dziko muno a Moses Kunkuyu wapempha dziko la Korea komanso mayiko amuno mu Africa kuti aganizire nkhani yokhudza njira za makono zomwe pachingerezi zimatchedwa kuti Information, Communication and Technology (ICT) ndicholinga chofuna kusintha miyoyo ya anthu amuno mu Africa. A Kunkuyu amayankhula izi m'dziko la Korea pamkumano […]
The post Tithandizeni ndi njira za makono za intaneti - Kunkuyu appeared first on Malawi 24.