Sukulu za pulayimale za boma zomwe ophunzira ake amuna anayamba kale kuvala ma yunifolomu a ma buluku, zachenjezedwa ndi unduna wa maphunziro kuti zisiye ponena kuti pakadali pano lamuloli silinakhazikitsidwe. Chaka chatha, phungu wa nyumba ya malamulo ochokera m’dera la Zomba Thondwe, a Roseby Gadama anapeleka maganizo m’nyumba ya malamulo kuti boma la Malawi liyambe […]
The post Sukulu za pulayimale zomwe ophunzira amuna akuvala ma buluku ngati yunifolomu azichenjeza appeared first on Malawi 24.